Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. Afilipi 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chitani zimenezi kuti muzitsimikizira kuti zinthu zofunika kwambiri ndi ziti,+ kuti mukhale opanda cholakwa+ ndi osakhumudwitsa+ ena kufikira tsiku la Khristu.
2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
10 Chitani zimenezi kuti muzitsimikizira kuti zinthu zofunika kwambiri ndi ziti,+ kuti mukhale opanda cholakwa+ ndi osakhumudwitsa+ ena kufikira tsiku la Khristu.