1 Akorinto 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno pa mapeto pake, adzapereka ufumu kwa Mulungu wake ndi Atate wake, atathetsa maboma onse, ulamuliro wonse, ndi mphamvu zonse.+ Akolose 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzera mwa iyeyo, inu simukusowa kalikonse. Iye ndiye mwini ulamuliro wonse ndi mphamvu zonse.+ Aheberi 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho iye wakhala woposa angelo,+ moti monga cholowa chake, walandira dzina+ lapamwamba kwambiri kuposa lawo.
24 Ndiyeno pa mapeto pake, adzapereka ufumu kwa Mulungu wake ndi Atate wake, atathetsa maboma onse, ulamuliro wonse, ndi mphamvu zonse.+
4 Choncho iye wakhala woposa angelo,+ moti monga cholowa chake, walandira dzina+ lapamwamba kwambiri kuposa lawo.