Aefeso 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anamuika pamwambamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, amphamvu onse, ambuye onse,+ ndi dzina lililonse loperekedwa kwa wina aliyense,+ osati mu nthawi* ino yokha,+ komanso imene ikubwerayo.+ 1 Petulo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ pakuti anapita kumwamba, ndipo angelo,+ maulamuliro, ndi mphamvu zinakhala pansi pake.+
21 Anamuika pamwambamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, amphamvu onse, ambuye onse,+ ndi dzina lililonse loperekedwa kwa wina aliyense,+ osati mu nthawi* ino yokha,+ komanso imene ikubwerayo.+
22 Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ pakuti anapita kumwamba, ndipo angelo,+ maulamuliro, ndi mphamvu zinakhala pansi pake.+