Mateyu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi. Aefeso 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo. Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.
18 Tsopano Yesu anayandikira ndi kulankhula nawo kuti: “Ulamuliro wonse+ waperekedwa kwa ine kumwamba ndi padziko lapansi.
23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo.
18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.