Afilipi 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho, pokhala wotsimikiza za chimenechi, ndikudziwa kuti ndikhalabe ndi moyo.+ Chotero ndidzakhala ndi inu nonse kuti mupite patsogolo,+ ndi kuti musangalale pa chikhulupiriro chanu. Filimoni 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni.
25 Choncho, pokhala wotsimikiza za chimenechi, ndikudziwa kuti ndikhalabe ndi moyo.+ Chotero ndidzakhala ndi inu nonse kuti mupite patsogolo,+ ndi kuti musangalale pa chikhulupiriro chanu.
22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni.