Aroma 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza ndikulakalaka kukuonani+ kuti ndikugawireni mphatso+ inayake yauzimu kuti mukhale olimba, Aefeso 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti awongolere oyerawo,+ achite ntchito yotumikira, amange thupi la Khristu,+ 1 Timoteyo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+
15 Sinkhasinkha zinthu zimenezi mozama.+ Dzipereke pa zinthu zimenezi kuti anthu onse aone kuti ukupita patsogolo.+