1 Atesalonika 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndi kuyembekezera+ Mwana wake kuchokera kumwamba,+ amene anamuukitsa kwa akufa.+ Mwanayo ndi Yesu, amene akutipulumutsa ku mkwiyo ukubwerawo.+ Aheberi 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+
10 ndi kuyembekezera+ Mwana wake kuchokera kumwamba,+ amene anamuukitsa kwa akufa.+ Mwanayo ndi Yesu, amene akutipulumutsa ku mkwiyo ukubwerawo.+
28 n’chimodzimodzinso Khristu. Iye anaperekedwa nsembe kamodzi+ kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Ndipo nthawi yachiwiri+ imene adzaonekere+ sadzaonekera n’cholinga chochotsa uchimo.+ Anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse ndi amene adzamuone.+