Yakobo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nanunso khalani oleza mtima.+ Limbitsani mitima yanu, chifukwa kukhalapo kwa Ambuye kwayandikira.+