Aefeso 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu. Aheberi 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+
13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu.
33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+