Machitidwe 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+ 1 Atesalonika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mukudziwa kuti choyamba titavutika+ ndi kuchitidwa zachipongwe+ ku Filipi,+ tinalimba mtima mothandizidwa ndi Mulungu wathu ndipo tinalankhula+ kwa inu uthenga wabwino wa Mulungu movutikira kwambiri. 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
22 Pamenepo khamu la anthu linanyamuka pamodzi ndi kuukira atumwiwo. Ndipo akuluakulu a boma aja, anavula atumwiwo malaya awo akunja mochita kuwang’ambira ndi kulamula kuti awakwapule ndi zikoti.+
2 Koma mukudziwa kuti choyamba titavutika+ ndi kuchitidwa zachipongwe+ ku Filipi,+ tinalimba mtima mothandizidwa ndi Mulungu wathu ndipo tinalankhula+ kwa inu uthenga wabwino wa Mulungu movutikira kwambiri.
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+