Aroma 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+ 1 Akorinto 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzauka,+ n’chifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa+ kuti akhale akufa?
4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+
29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzauka,+ n’chifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa+ kuti akhale akufa?