Aefeso 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Akazi agonjere+ amuna awo ngati mmene amagonjerera Ambuye, 1 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+
3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+