Akolose 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu akazi, muzigonjera+ amuna anu, pakuti zimenezi ndiye zoyenera kwa anthu otsatira Ambuye. Tito 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+ 1 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+
5 kukhala oganiza bwino, oyera,+ ogwira ntchito zapakhomo, abwino ndi ogonjera+ amuna awo, kuti mawu a Mulungu asanyozedwe.+
3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+