Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse, osaleka.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani ndi chiyembekezocho.+ Pirirani chisautso.+ Limbikirani kupemphera.+ Aefeso 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene mukutero, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ mwa mtundu uliwonse wa pemphero+ ndi pembedzero. Kuti muchite zimenezi, khalani maso mosalekeza ndi kupemphera mopembedzera m’malo mwa oyera onse,
18 Pamene mukutero, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ mwa mtundu uliwonse wa pemphero+ ndi pembedzero. Kuti muchite zimenezi, khalani maso mosalekeza ndi kupemphera mopembedzera m’malo mwa oyera onse,