2 Akorinto 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ngati tili m’masautso, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe ndi kupulumutsidwa.+ Ngati tikutonthozedwa, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe kuti mupirire masautso amene ifenso tikukumana nawo.+
6 Tsopano ngati tili m’masautso, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe ndi kupulumutsidwa.+ Ngati tikutonthozedwa, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe kuti mupirire masautso amene ifenso tikukumana nawo.+