2Chotero abale, pamene ndinafika kwa inu kudzalengeza za chinsinsi chopatulika+ cha Mulungu, sindinafike ndi malankhulidwe+ adzaoneni kapena ndi nzeru zodabwitsa.
6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino.