Deuteronomo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Usalakelake mkazi wa mnzako.+ Usalakelake mwadyera nyumba ya mnzako, munda wake, kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzako.’+ 1 Akorinto 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’malomwake, inuyo mumachita zolakwa ndiponso mumabera ena, ndipo abale anu ndi amene mumawachitira zimenezi.+ 1 Akorinto 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma chifukwa cha kuwanda kwa dama,*+ mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake.
21 “‘Usalakelake mkazi wa mnzako.+ Usalakelake mwadyera nyumba ya mnzako, munda wake, kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ng’ombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzako.’+
8 M’malomwake, inuyo mumachita zolakwa ndiponso mumabera ena, ndipo abale anu ndi amene mumawachitira zimenezi.+
2 Koma chifukwa cha kuwanda kwa dama,*+ mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake.