Aheberi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+ 1 Petulo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikukulemberani inu amene Mulungu Atate+ anakudziwiranitu mwa kukuyeretsani ndi mzimu+ kuti mukhale omvera ndi owazidwa+ magazi a Yesu Khristu, kuti:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere ziwonjezeke kwa inu.+
11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+
2 Ndikukulemberani inu amene Mulungu Atate+ anakudziwiranitu mwa kukuyeretsani ndi mzimu+ kuti mukhale omvera ndi owazidwa+ magazi a Yesu Khristu, kuti:+ Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere ziwonjezeke kwa inu.+