Aroma 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+ Yakobo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu. 1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+
8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+
8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu.
22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+