Aroma 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+ 1 Atesalonika 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Abale, pitirizani kutipempherera.+ Aheberi 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pitirizani kutipempherera,+ pakuti tikukhulupirira kuti tili ndi chikumbumtima choona, popeza tikufuna kuchita zinthu zonse moona mtima.+
30 Chotero ndikukudandaulirani abale, kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi mwa chikondi cha mzimu,+ kuti mulimbikire limodzi ndi ine popemphera kwa Mulungu za ineyo.+
18 Pitirizani kutipempherera,+ pakuti tikukhulupirira kuti tili ndi chikumbumtima choona, popeza tikufuna kuchita zinthu zonse moona mtima.+