Mateyu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ 1 Akorinto 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kapena kodi ine ndi Baranaba+ ndife tokha amene tilibe ufulu wosiya kugwira ntchito yakuthupi?+
10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+