1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, monga mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ Afilipi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mogwirizana, khalani otsanzira+ ine abale, ndipo muzionetsetsa amene akuyenda mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.+
17 Mogwirizana, khalani otsanzira+ ine abale, ndipo muzionetsetsa amene akuyenda mogwirizana ndi chitsanzo chimene tinakupatsani.+