1 Akorinto 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero ndikukuchondererani, tsanzirani ineyo.+ 2 Atesalonika 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sikuti tinatero chifukwa chopanda ulamuliro,+ koma kuti tikhale chitsanzo kwa inu, kuti inu mutitsanzire.+
9 Sikuti tinatero chifukwa chopanda ulamuliro,+ koma kuti tikhale chitsanzo kwa inu, kuti inu mutitsanzire.+