1 Akorinto 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ngati munthu akuganiza kuti ndi mneneri kapena ali ndi mphatso ya mzimu, avomereze zimene ndakulemberanizi, chifukwa ndizo lamulo la Ambuye.+ 1 Akorinto 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+ 1 Atesalonika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.
37 Ngati munthu akuganiza kuti ndi mneneri kapena ali ndi mphatso ya mzimu, avomereze zimene ndakulemberanizi, chifukwa ndizo lamulo la Ambuye.+
16 Tsopano ponena za chopereka+ chopita kwa oyerawo,+ inunso tsatirani malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.+
11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.