Aroma 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuti mwina ndingapangitse anthu a mtundu wanga kuchita nsanje ndi kupulumutsapo+ ena a iwo.+ 1 Akorinto 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena. 1 Petulo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma vomerezani m’mitima mwanu kuti Khristu ndi Ambuye ndiponso kuti ndi woyera.+ Khalani okonzeka nthawi zonse kuyankha+ aliyense amene wakufunsani za chiyembekezo chimene muli nacho, koma ayankheni ndi mtima wofatsa+ ndiponso mwaulemu kwambiri.
22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena.
15 Koma vomerezani m’mitima mwanu kuti Khristu ndi Ambuye ndiponso kuti ndi woyera.+ Khalani okonzeka nthawi zonse kuyankha+ aliyense amene wakufunsani za chiyembekezo chimene muli nacho, koma ayankheni ndi mtima wofatsa+ ndiponso mwaulemu kwambiri.