1 Timoteyo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, aziwathandiza,+ kuti akazi amasiyewo asakhale cholemetsa ku mpingo. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, aziwathandiza,+ kuti akazi amasiyewo asakhale cholemetsa ku mpingo. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.+
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+