Mateyu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kapolo sangatumikire ambuye awiri, pakuti adzadana ndi mmodzi ndi kukonda winayo,+ kapena adzakhulupirika kwa mmodzi ndi kunyoza winayo. Simungathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.+ Luka 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti kumene kuli chuma chanu, mitima yanunso idzakhala komweko.+ Aheberi 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+
24 “Kapolo sangatumikire ambuye awiri, pakuti adzadana ndi mmodzi ndi kukonda winayo,+ kapena adzakhulupirika kwa mmodzi ndi kunyoza winayo. Simungathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.+
12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+