Yohane 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo unakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo moyowo unali kuwala+ kounikira anthu. Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+ 1 Yohane 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+
24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+
2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+