1 Akorinto 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+ Agalatiya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+
14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+
6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+
16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+