Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 asalemekeze bambo ake.’+ Chotero mwasandutsa mawu a Mulungu kukhala opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+

  • Machitidwe 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano atumwi ndi abale amene anali mu Yudeya anamva kuti anthu a mitundu ina+ nawonso alandira mawu a Mulungu.

  • 1 Atesalonika 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithudi, n’chifukwa chake ifenso timayamikadi+ Mulungu mosalekeza. Pakuti pamene munalandira mawu a Mulungu+ amene munamva kwa ife, simunawalandire monga mawu a anthu+ ayi, koma mmene alilidi, monga mawu a Mulungu. Mawu amenewa akugwiranso ntchito mwa inu okhulupirira.+

  • 1 Atesalonika 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti tikukuuzani izi mogwirizana ndi mawu a Yehova+ kuti, ife amoyofe amene tidzakhalapo pa nthawi ya kukhalapo* kwa Ambuye,+ sitidzakhala patsogolo pa amene agona mu imfa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena