Numeri 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo. Yoswa 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika m’manda m’phiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa m’dera lamapiri la Efuraimu.
28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe n’kuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika m’phirimo.
33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika m’manda m’phiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa m’dera lamapiri la Efuraimu.