Aheberi 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero mzimu woyera ukuonetsa poyera kuti njira+ yolowera kumalo oyera amkatikati inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+ Aheberi 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+
8 Chotero mzimu woyera ukuonetsa poyera kuti njira+ yolowera kumalo oyera amkatikati inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+
24 Pakuti Khristu sanalowe m’malo oyera amkatikati opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Tsopano ali kumwamba kuti aonekere pamaso pa Mulungu chifukwa cha ife.+