Levitiko 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.
38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.