Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kholo lakolo ndinalisankha kuchokera m’mafuko onse a Isiraeli kuti akhale wansembe wanga,+ ndipo azikwera paguwa langa lansembe+ kuti utsi wa nsembezo uzikwera kumwamba, kutinso azivala efodi pamaso panga. Ndinachita izi kuti ndipatse nyumba ya kholo lako nsembe zonse zotentha ndi moto za ana a Isiraeli.+

  • 1 Mbiri 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Limeneli ndilo linali dongosolo+ la utumiki wawo,+ kuti azilowa m’nyumba ya Yehova malinga ndi mphamvu imene anapatsidwa+ kudzera m’dzanja la Aroni kholo lawo, monga mmene Yehova Mulungu wa Isiraeli anamulamulira.

  • 2 Mbiri 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno inu ana anga musapumule,+ chifukwa inu ndi amene Yehova wakusankhani kuti muziima pamaso pake ndi kum’tumikira+ ndiponso kuti mukhalebe atumiki ake+ ndi ofukiza nsembe yautsi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena