Ekisodo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mukatero mutenge kamtengo ka hisope+ n’kukaviika m’beseni la magazi ndi kuwaza pafelemu la pamwamba pa chitseko, ndipo ena mwa magaziwo muwaze pamafelemu awiri a m’mbali mwa khomo. Aliyense asatuluke m’nyumba yake mpaka m’mawa.
22 Mukatero mutenge kamtengo ka hisope+ n’kukaviika m’beseni la magazi ndi kuwaza pafelemu la pamwamba pa chitseko, ndipo ena mwa magaziwo muwaze pamafelemu awiri a m’mbali mwa khomo. Aliyense asatuluke m’nyumba yake mpaka m’mawa.