Ekisodo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Yehova akamapita kukapha Aiguputo ndi mliri, akaona magazi pamafelemu a pamwamba pa zitseko zanu ndi mafelemu awiri a m’mbali mwa khomo, Yehova adzapitirira khomo limenelo ndipo sadzalola chiwonongeko kulowa m’nyumba zanu ndi kukuphani.+
23 Pamenepo Yehova akamapita kukapha Aiguputo ndi mliri, akaona magazi pamafelemu a pamwamba pa zitseko zanu ndi mafelemu awiri a m’mbali mwa khomo, Yehova adzapitirira khomo limenelo ndipo sadzalola chiwonongeko kulowa m’nyumba zanu ndi kukuphani.+