Yesaya 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+ Ezekieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+ Aheberi 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwa chikhulupiriro, iye anachita pasika+ ndiponso anawaza magazi pamafelemu a pakhomo,+ kuti wowonongayo asakhudze ana awo oyamba kubadwa.+
36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+
6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+
28 Mwa chikhulupiriro, iye anachita pasika+ ndiponso anawaza magazi pamafelemu a pakhomo,+ kuti wowonongayo asakhudze ana awo oyamba kubadwa.+