Aroma 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amakhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake+ kuti akhale wolungama, koma ndi pakamwa pake amalengeza poyera+ chikhulupiriro chake kuti apulumuke. Yakobo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Momwemonso chikhulupiriro pachokha, ngati chilibe ntchito zake,+ ndi chakufa.
10 Munthu amakhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake+ kuti akhale wolungama, koma ndi pakamwa pake amalengeza poyera+ chikhulupiriro chake kuti apulumuke.