Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+Koma wodzikuza samuyandikira.+ Yesaya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
11 Maso odzikuza a munthu wochokera kufumbi adzatsika, ndipo anthu odzikweza adzawerama.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+