Levitiko 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova. Miyambo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
16 “‘Usamayendeyende pakati pa anthu amtundu wako n’kumachita miseche.+ Usachite kanthu kalikonse kuti uphetse mnzako.+ Ine ndine Yehova.
9 Wophimba machimo akufunafuna chikondi,+ ndipo amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+