Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+ 1 Yohane 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano inu ana anga okondedwa,+ khalanibe ogwirizana+ naye, kuti akadzaonetsedwa,+ tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Kutinso tisadzachititsidwe manyazi ndi kuchotsedwa kwa iye pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.
16 Choncho, tiyeni tiyandikire mpando wachifumu wa kukoma mtima kwakukulu ndipo tipemphere kwa Mulungu+ ndi ufulu wa kulankhula,+ kuti atichitire chifundo ndi kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi imene tikufunika thandizo.+
28 Tsopano inu ana anga okondedwa,+ khalanibe ogwirizana+ naye, kuti akadzaonetsedwa,+ tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Kutinso tisadzachititsidwe manyazi ndi kuchotsedwa kwa iye pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.