Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?

  • Maliko 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+

  • Agalatiya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 iwo atazindikira kukoma mtima kwakukulu+ kumene ndinapatsidwa,+ Yakobo,+ Kefa ndi Yohane, amene anali ngati mizati,+ anagwira chanza ineyo ndi Baranaba.+ Anatero posonyeza kuti agwirizana nazo+ zoti ife tipite kwa anthu a mitundu ina, ndipo iwo apite kwa odulidwa.

  • Yakobo 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Ine Yakobo,+ kapolo+ wa Mulungu ndi wa Ambuye Yesu Khristu, ndikupereka moni kwa mafuko 12+ amene ali obalalika:+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena