Mateyu 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+
31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+
22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+