Chivumbulutso 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’dzanja lake, anali ndi mpukutu waung’ono wofunyulula. Iye anaponda panyanja ndi phazi lake lamanja, koma ndi phazi lake lamanzere anaponda pamtunda.+
2 M’dzanja lake, anali ndi mpukutu waung’ono wofunyulula. Iye anaponda panyanja ndi phazi lake lamanja, koma ndi phazi lake lamanzere anaponda pamtunda.+