Yeremiya 51:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.
34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.