Yohane 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso, iye sanafunikire wina woti achite kumuuza za munthu, chifukwa payekha anali kudziwa zimene zili m’mitima ya anthu.+ Chivumbulutso 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Ndikudziwa ntchito zako, chikondi chako,+ chikhulupiriro chako, utumiki wako, ndi kupirira kwako. Ndikudziwanso kuti ntchito zako+ zapanopa n’zambiri kuposa zoyamba zija.+ Chivumbulutso 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+
25 Komanso, iye sanafunikire wina woti achite kumuuza za munthu, chifukwa payekha anali kudziwa zimene zili m’mitima ya anthu.+
19 ‘Ndikudziwa ntchito zako, chikondi chako,+ chikhulupiriro chako, utumiki wako, ndi kupirira kwako. Ndikudziwanso kuti ntchito zako+ zapanopa n’zambiri kuposa zoyamba zija.+
3 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Sade, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena iye amene ali ndi mizimu 7+ ya Mulungu, ndi nyenyezi 7.+ ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti uli ndi dzina lakuti uli moyo, pamene ndiwe wakufa.+