1 Akorinto 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo! Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+
15 Kodi simukudziwa kuti matupi anu ndiwo ziwalo+ za Khristu?+ Ndiye kodi ine nditenge ziwalo za Khristu n’kuzisandutsa ziwalo za hule?+ Zosatheka zimenezo!
4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+