Ezekieli 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+
33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+