-
Genesis 35:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ana amene Rakele anaberekera Yakobo anali Yosefe ndi Benjamini.
-
-
Deuteronomo 33:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
“Dziko lake lidalitsidwe ndi Yehova.+
Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba,
Ndi mame komanso madzi ochokera mu akasupe a pansi pa nthaka.+
-