Ekisodo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno upange bwalo+ la chihema. Kumbali yakumʼmwera, bwalolo ulitchinge ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo ukhale mamita 45 mulitali mwake kumbali imodziyo.+ Ekisodo 38:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo.+ Kumbali yakumʼmwera ya bwalolo anapangako mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mamita 45 mulitali mwake.+
9 Ndiyeno upange bwalo+ la chihema. Kumbali yakumʼmwera, bwalolo ulitchinge ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo ukhale mamita 45 mulitali mwake kumbali imodziyo.+
9 Ndiyeno anapanga bwalo.+ Kumbali yakumʼmwera ya bwalolo anapangako mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri. Mpandawo unali mamita 45 mulitali mwake.+